Salimo 69:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ine ndinali kupemphera kwa inu Yehova,+Pa nthawi yovomerezedwa, inu Mulungu.+Ndiyankheni mwa kuchuluka kwa kukoma mtima kwanu kosatha, ndipo sonyezani kuti ndinudi mpulumutsi.+ Zekariya 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taonani mwala+ umene ndauika pamaso pa Yoswa. Mwala umenewu uli ndi maso 7.+ Pamwalawu ndilembapo zinthu mochita kugoba,+ ndipo ndidzachotsa zolakwa za dzikoli m’tsiku limodzi,’+ watero Yehova wa makamu. 2 Akorinto 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti iye anati: “Pa nthawi yovomerezedwa ndinakumvera, ndipo m’tsiku lachipulumutso ndinakuthandiza.”+ Ndithudi, inoyo ndiyo nthawi yeniyeni yovomerezedwa.+ Linolo ndilo tsiku lachipulumutso.+
13 Koma ine ndinali kupemphera kwa inu Yehova,+Pa nthawi yovomerezedwa, inu Mulungu.+Ndiyankheni mwa kuchuluka kwa kukoma mtima kwanu kosatha, ndipo sonyezani kuti ndinudi mpulumutsi.+
9 Taonani mwala+ umene ndauika pamaso pa Yoswa. Mwala umenewu uli ndi maso 7.+ Pamwalawu ndilembapo zinthu mochita kugoba,+ ndipo ndidzachotsa zolakwa za dzikoli m’tsiku limodzi,’+ watero Yehova wa makamu.
2 Pakuti iye anati: “Pa nthawi yovomerezedwa ndinakumvera, ndipo m’tsiku lachipulumutso ndinakuthandiza.”+ Ndithudi, inoyo ndiyo nthawi yeniyeni yovomerezedwa.+ Linolo ndilo tsiku lachipulumutso.+