Ekisodo 28:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ugwiritse ntchito mmisiri wogoba kuti alembe mayina a ana a Isiraeli pamiyala iwiriyo mwaluso la wogoba miyala.+ Awalembe ngati mmene amagobera chidindo. Apange miyalayo moti izitha kulowa m’zoikamo zake zagolide.+ Yohane 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Musamagwire ntchito kuti mungopeza chakudya chimene chimawonongeka,+ koma kuti mupeze chakudya chokhalitsa, chopereka moyo wosatha,+ chimene Mwana wa munthu adzakupatsani. Pakuti Atate, Mulungu yekhayo, waika chisindikizo pa iye chomuvomereza.”+
11 Ugwiritse ntchito mmisiri wogoba kuti alembe mayina a ana a Isiraeli pamiyala iwiriyo mwaluso la wogoba miyala.+ Awalembe ngati mmene amagobera chidindo. Apange miyalayo moti izitha kulowa m’zoikamo zake zagolide.+
27 Musamagwire ntchito kuti mungopeza chakudya chimene chimawonongeka,+ koma kuti mupeze chakudya chokhalitsa, chopereka moyo wosatha,+ chimene Mwana wa munthu adzakupatsani. Pakuti Atate, Mulungu yekhayo, waika chisindikizo pa iye chomuvomereza.”+