Yohane 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma amene adzamwa madzi amene ine ndidzam’patse sadzamvanso ludzu m’pang’ono pomwe.+ Ndipo madzi amene ndidzam’patse, adzasanduka kasupe wa madzi+ otuluka mwa iye, opatsa moyo wosatha.”+ Yohane 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+ Aroma 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa malipiro a uchimo ndi imfa,+ koma mphatso+ imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha+ kudzera mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.+
14 Koma amene adzamwa madzi amene ine ndidzam’patse sadzamvanso ludzu m’pang’ono pomwe.+ Ndipo madzi amene ndidzam’patse, adzasanduka kasupe wa madzi+ otuluka mwa iye, opatsa moyo wosatha.”+
3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+
23 Chifukwa malipiro a uchimo ndi imfa,+ koma mphatso+ imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha+ kudzera mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.+