Salimo 118:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwala umene omanga nyumba anaukana+Wakhala mwala wofunika kwambiri wapakona.+ Yesaya 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndikuika mwala mu Ziyoni+ kuti ukhale maziko. Umenewu ndi mwala+ wapakona woyesedwa,+ wamtengo wapatali,+ woti ukhale maziko olimba.+ Palibe munthu woukhulupirira amene adzade nkhawa.+ Mateyu 21:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiyeno Yesu anawafunsa kuti: “Kodi simunawerenge zimene Malemba amanena zakuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana+ ndi umene wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.+ Umenewu wachokera kwa Yehova, ndipo ndi wodabwitsa m’maso mwathu’? 1 Petulo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene mukubwera kwa iye, amene ndiye mwala wamoyo+ umene anthu+ anaukana,+ koma umene Mulungu anausankha, umenenso uli wamtengo wapatali kwa iye,+
16 Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndikuika mwala mu Ziyoni+ kuti ukhale maziko. Umenewu ndi mwala+ wapakona woyesedwa,+ wamtengo wapatali,+ woti ukhale maziko olimba.+ Palibe munthu woukhulupirira amene adzade nkhawa.+
42 Ndiyeno Yesu anawafunsa kuti: “Kodi simunawerenge zimene Malemba amanena zakuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana+ ndi umene wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.+ Umenewu wachokera kwa Yehova, ndipo ndi wodabwitsa m’maso mwathu’?
4 Pamene mukubwera kwa iye, amene ndiye mwala wamoyo+ umene anthu+ anaukana,+ koma umene Mulungu anausankha, umenenso uli wamtengo wapatali kwa iye,+