Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 8:66
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 66 Pa tsiku la 8 Solomo anauza anthuwo kuti azipita,+ ndipo anthuwo anadalitsa mfumuyo n’kuyamba kupita kwawo. Anapita akusangalala,+ chimwemwe chitadzaza mumtima,+ chifukwa cha zabwino zonse+ zimene Yehova anachitira Davide mtumiki wake ndi anthu ake Aisiraeli.

  • Esitere 8:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakati pa Ayuda panali chisangalalo, kukondwa+ ndi kunyadira ndipo anthu anali kuwapatsa ulemu.

  • Yohane 16:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Choncho inunso muli ndi chisoni panopa. Koma ndidzakuonaninso, ndipo mitima yanu idzasangalala.+ Palibenso amene adzathetse chimwemwe chanu.

  • Machitidwe 5:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Choncho atumwiwo anachoka pamaso pa Khoti Lalikulu la Ayuda, ali osangalala+ chifukwa chakuti Mulungu anawaona kuti ndi oyenera kuchitiridwa chipongwe chifukwa cha dzina la Yesu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena