Salimo 119:151 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 151 Inu Yehova muli pafupi,+Ndipo malamulo anu onse ndi choonadi.+