Salimo 119:175 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 175 Ndisungenibe wamoyo kuti ndikutamandeni,+Zigamulo zanu zindithandize.+