Salimo 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndichitireni zimenezi kuti ndilengeze ntchito zanu zonse zotamandika+Pazipata+ za mwana wamkazi wa Ziyoni,+Kuti ndikondwere ndi chipulumutso chanu.+ Yesaya 38:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu wamoyo, amene akupuma, ndi amene angakutamandeni,+Ngati mmene ineyo ndikuchitira lero.+Bambo akhoza kuphunzitsa+ ana ake za kukhulupirika kwanu.
14 Ndichitireni zimenezi kuti ndilengeze ntchito zanu zonse zotamandika+Pazipata+ za mwana wamkazi wa Ziyoni,+Kuti ndikondwere ndi chipulumutso chanu.+
19 Munthu wamoyo, amene akupuma, ndi amene angakutamandeni,+Ngati mmene ineyo ndikuchitira lero.+Bambo akhoza kuphunzitsa+ ana ake za kukhulupirika kwanu.