Salimo 140:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikudziwa bwino kwambiri kuti Yehova adzazengera+Mlandu anthu osautsika. Iye adzachitira chilungamo anthu osauka.+
12 Ndikudziwa bwino kwambiri kuti Yehova adzazengera+Mlandu anthu osautsika. Iye adzachitira chilungamo anthu osauka.+