Miyambo 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu osadziwa zinthu, ndithu adzakhala opusa,+ koma kwa ochenjera, kudziwa zinthu kudzakhala ngati chovala cha kumutu.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:18 Nsanja ya Olonda,7/15/2005, tsa. 19
18 Anthu osadziwa zinthu, ndithu adzakhala opusa,+ koma kwa ochenjera, kudziwa zinthu kudzakhala ngati chovala cha kumutu.+