Miyambo 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amene akuteteza mtengo wa mkuyu adzadya zipatso zake,+ ndipo amene akuteteza mbuye wake adzalemekezedwa.+
18 Amene akuteteza mtengo wa mkuyu adzadya zipatso zake,+ ndipo amene akuteteza mbuye wake adzalemekezedwa.+