Miyambo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Waulesi amalakalaka zinthu, chonsecho moyo wake ulibe chilichonse.+ Koma anthu akhama adzanenepa.+ 1 Akorinto 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Alipo kodi msilikali amene amatumikira, koma n’kumadzilipira yekha? Ndani amalima munda wa mpesa koma osadya zipatso zake?+ Kapena ndani amaweta ziweto koma osamwako mkaka wake?+
7 Alipo kodi msilikali amene amatumikira, koma n’kumadzilipira yekha? Ndani amalima munda wa mpesa koma osadya zipatso zake?+ Kapena ndani amaweta ziweto koma osamwako mkaka wake?+