Deuteronomo 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kodi pali amene walima munda wa mpesa koma sanayambe kukolola zipatso zake? Achoke ndi kubwerera kunyumba yake, kuopera kuti angafe pankhondo ndipo munthu wina angakolole za m’munda wakewo.+ Miyambo 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amene akuteteza mtengo wa mkuyu adzadya zipatso zake,+ ndipo amene akuteteza mbuye wake adzalemekezedwa.+
6 Kodi pali amene walima munda wa mpesa koma sanayambe kukolola zipatso zake? Achoke ndi kubwerera kunyumba yake, kuopera kuti angafe pankhondo ndipo munthu wina angakolole za m’munda wakewo.+
18 Amene akuteteza mtengo wa mkuyu adzadya zipatso zake,+ ndipo amene akuteteza mbuye wake adzalemekezedwa.+