Miyambo 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzapeza madalitso ambiri,+ koma woyesetsa kuti apeze chuma mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:20 Nsanja ya Olonda,11/15/1986, tsa. 30
20 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzapeza madalitso ambiri,+ koma woyesetsa kuti apeze chuma mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+