Mlaliki 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndinapereka mtima wanga kuti udziwe nzeru ndiponso misala,+ ndipo ndadziwa uchitsiru.+ Pochita zimenezi ndazindikira kuti zimenezinso zili ngati kuthamangitsa mphepo.+
17 Ndinapereka mtima wanga kuti udziwe nzeru ndiponso misala,+ ndipo ndadziwa uchitsiru.+ Pochita zimenezi ndazindikira kuti zimenezinso zili ngati kuthamangitsa mphepo.+