Mlaliki 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale munthu atakhala ndi moyo zaka zambiri, m’zaka zonsezo azisangalala.+ Iye akumbukire masiku a mdima,+ ngakhale atakhala ambiri. Tsiku lililonse limene likubwera n’lachabechabe.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:8 Nsanja ya Olonda,11/1/2006, tsa. 158/15/1998, tsa. 9
8 Ngakhale munthu atakhala ndi moyo zaka zambiri, m’zaka zonsezo azisangalala.+ Iye akumbukire masiku a mdima,+ ngakhale atakhala ambiri. Tsiku lililonse limene likubwera n’lachabechabe.+