Nyimbo ya Solomo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Alonda+ amene anali kuzungulira mumzindawo anandipeza, ndipo ine ndinawafunsa kuti: ‘Kodi amuna inu, mwamuonako munthu amene mtima wanga umam’konda?’
3 Alonda+ amene anali kuzungulira mumzindawo anandipeza, ndipo ine ndinawafunsa kuti: ‘Kodi amuna inu, mwamuonako munthu amene mtima wanga umam’konda?’