Nyimbo ya Solomo 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yang’ana kumbali kuti maso ako+ asandiyang’anitsitse, chifukwa akundichititsa mantha. Tsitsi lako likuoneka ngati gulu la mbuzi zimene zikudumphadumpha potsetsereka kuchokera ku Giliyadi.+ Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:5 Nsanja ya Olonda,11/15/2006, tsa. 19
5 Yang’ana kumbali kuti maso ako+ asandiyang’anitsitse, chifukwa akundichititsa mantha. Tsitsi lako likuoneka ngati gulu la mbuzi zimene zikudumphadumpha potsetsereka kuchokera ku Giliyadi.+