Nyimbo ya Solomo 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zipatso za mandereki*+ zikununkhira, ndipo pafupi ndi makomo olowera kunyumba zathu pali zipatso zosiyanasiyana zokoma kwambiri.+ Ndakusungira zipatso zatsopano ndi zakale zomwe, iwe wachikondi wanga.
13 Zipatso za mandereki*+ zikununkhira, ndipo pafupi ndi makomo olowera kunyumba zathu pali zipatso zosiyanasiyana zokoma kwambiri.+ Ndakusungira zipatso zatsopano ndi zakale zomwe, iwe wachikondi wanga.