Nyimbo ya Solomo 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zipatso za mandereki*+ zikununkhira,Pamakomo olowera kunyumba zathu pali zipatso zosiyanasiyana zokoma kwambiri.+ Ndakusungira zipatso zatsopano ndi zakale zomwe,Iwe wachikondi wanga.”
13 Zipatso za mandereki*+ zikununkhira,Pamakomo olowera kunyumba zathu pali zipatso zosiyanasiyana zokoma kwambiri.+ Ndakusungira zipatso zatsopano ndi zakale zomwe,Iwe wachikondi wanga.”