Yesaya 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti mwawanyanyala anthu anu, nyumba ya Yakobo.+ Iwo adzaza ndi zinthu zochokera Kum’mawa.+ Akuchita zamatsenga+ ngati Afilisiti ndiponso ali ndi ana ambiri a alendo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:6 Yesaya 1, ptsa. 49-50
6 Pakuti mwawanyanyala anthu anu, nyumba ya Yakobo.+ Iwo adzaza ndi zinthu zochokera Kum’mawa.+ Akuchita zamatsenga+ ngati Afilisiti ndiponso ali ndi ana ambiri a alendo.+