Yesaya 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti goli la katundu wawo,+ ndodo yomwe inali pamapewa awo, ndiponso ndodo ya amene anali kuwakusira ku ntchito,+ mwazithyolathyola ngati pa tsiku limene Amidiyani anagonjetsedwa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:4 Yesaya 1, ptsa. 128-129
4 Pakuti goli la katundu wawo,+ ndodo yomwe inali pamapewa awo, ndiponso ndodo ya amene anali kuwakusira ku ntchito,+ mwazithyolathyola ngati pa tsiku limene Amidiyani anagonjetsedwa.+