Yesaya 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anthu inu, tumizani nkhosa yamphongo kwa wolamulira wa dziko.+ Muitumize kuchokera ku Sela kudutsa kuchipululu mpaka kukafika kuphiri la mwana wamkazi wa Ziyoni.+
16 Anthu inu, tumizani nkhosa yamphongo kwa wolamulira wa dziko.+ Muitumize kuchokera ku Sela kudutsa kuchipululu mpaka kukafika kuphiri la mwana wamkazi wa Ziyoni.+