Yesaya 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kukadali masana, iye aima ku Nobu.+ Ndi dzanja lake, iye akuopseza phiri la mwana wamkazi wa Ziyoni, phiri limene pali Yerusalemu.+ Mika 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma iwe nsanja ya gulu la nkhosa, malo okwera a mwana wamkazi wa Ziyoni,+ ulamuliro udzabwerera kwa iwe. Ulamuliro woyamba, ufumu wa mwana wamkazi wa Yerusalemu,+ udzabwerera kwa iwe.+
32 Kukadali masana, iye aima ku Nobu.+ Ndi dzanja lake, iye akuopseza phiri la mwana wamkazi wa Ziyoni, phiri limene pali Yerusalemu.+
8 “Koma iwe nsanja ya gulu la nkhosa, malo okwera a mwana wamkazi wa Ziyoni,+ ulamuliro udzabwerera kwa iwe. Ulamuliro woyamba, ufumu wa mwana wamkazi wa Yerusalemu,+ udzabwerera kwa iwe.+