Yesaya 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mitsinje idzanunkha. Ngalande za ku Iguputo zochokera mumtsinje wa Nailo zidzaphwa ndipo zidzauma.+ Bango+ ndi udzu* zidzafota.
6 Mitsinje idzanunkha. Ngalande za ku Iguputo zochokera mumtsinje wa Nailo zidzaphwa ndipo zidzauma.+ Bango+ ndi udzu* zidzafota.