Yesaya 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu otsala pa amuna oponya mivi ndi uta, omwe ndi amuna amphamvu a ana a Kedara, adzakhala ochepa,+ pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena zimenezi.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:17 Yesaya 1, ptsa. 228-229
17 Anthu otsala pa amuna oponya mivi ndi uta, omwe ndi amuna amphamvu a ana a Kedara, adzakhala ochepa,+ pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena zimenezi.”+