Yeremiya 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno ukapite kuchigwa cha mwana wa Hinomu,+ chimene chili pafupi ndi khomo la Chipata cha Mapale.* Kumeneko ukanene mawu onse amene ndikuuze.+
2 Ndiyeno ukapite kuchigwa cha mwana wa Hinomu,+ chimene chili pafupi ndi khomo la Chipata cha Mapale.* Kumeneko ukanene mawu onse amene ndikuuze.+