Yeremiya 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Taonani! Nyundo yophwanyira mitundu+ ya anthu padziko lonse lapansi yathyoledwa ndipo yawonongeka.+ Taonani! Babulo wakhala chinthu chodabwitsa pakati pa mitundu ina.+
23 Taonani! Nyundo yophwanyira mitundu+ ya anthu padziko lonse lapansi yathyoledwa ndipo yawonongeka.+ Taonani! Babulo wakhala chinthu chodabwitsa pakati pa mitundu ina.+