Maliro 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ife takhala anthu amasiye opanda bambo.+ Amayi athu akhala ngati akazi amasiye.+