Ezekieli 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzakusiya pamtunda ndiponso ndidzakuponya kuchigwa.+ Ndidzachititsa kuti zolengedwa zonse zouluka m’mlengalenga zitere pa iwe. Ndidzakhutitsa zilombo zakutchire ndi nyama yako.+
4 Ndidzakusiya pamtunda ndiponso ndidzakuponya kuchigwa.+ Ndidzachititsa kuti zolengedwa zonse zouluka m’mlengalenga zitere pa iwe. Ndidzakhutitsa zilombo zakutchire ndi nyama yako.+