Ezekieli 32:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “‘Kumeneko n’kumene kuli Edomu,+ mafumu ake ndi atsogoleri ake onse. Amenewa anaikidwa m’manda akadali amphamvu. Anaikidwa pamodzi ndi ophedwa ndi lupanga.+ Iwo adzagona limodzi ndi anthu osadulidwa+ komanso anthu amene akutsikira kudzenje.
29 “‘Kumeneko n’kumene kuli Edomu,+ mafumu ake ndi atsogoleri ake onse. Amenewa anaikidwa m’manda akadali amphamvu. Anaikidwa pamodzi ndi ophedwa ndi lupanga.+ Iwo adzagona limodzi ndi anthu osadulidwa+ komanso anthu amene akutsikira kudzenje.