Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 25:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndiyeno Esau anapempha Yakobo kuti: “Chonde, fulumira ndipatseko chakudya chofiiracho pang’ono, icho chofiiracho! Ndatopatu ine!” Ndiye chifukwa chake anatchedwa Edomu.*+

  • Genesis 36:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Mbiri ya Esau, kapena kuti Edomu,+ ili motere:

  • Yesaya 34:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Pakuti lupanga langa+ lidzakhala magazi okhaokha kumwambako. Lupangalo lidzatsikira pa Edomu+ ndi pa anthu amene ndikufuna kuwawononga+ mogwirizana ndi chilungamo changa.

  • Ezekieli 25:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti Edomu walanga nyumba ya Yuda ndipo akupitiriza kuilanga ndi kuichitira zinthu zoipa kwambiri,+

  • Amosi 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Yehova wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti Edomu wandipandukira mobwerezabwereza,+ sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anathamangitsa m’bale wake ndi lupanga,+ sanasonyeze chifundo,+ akupitiriza kukhadzulakhadzula zinthu ali wokwiya komanso akukhalabe wokwiya mosalekeza.+

  • Obadiya 1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Tsopano awa ndiwo masomphenya a Obadiya:

      Zimene Yehova Ambuye Wamkulu Koposa wanena zokhudza Edomu ndi izi:+ “Ife tamva uthenga wochokera kwa Yehova ndipo nthumwi yatumidwa kwa anthu a mitundu ina kukanena kuti: ‘Nyamukani anthu inu, tiyeni timuukire ndi kumenyana naye.’”+

  • Malaki 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Popeza kuti Edomu akunena kuti, ‘Ife tawonongedwa, koma tibwerera ndi kukamanga malo athu owonongedwawo,’ Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Iwo akamanga, koma ine ndikagwetsa.+ Anthu adzatcha malo awowo, “dera la zoipa” ndipo iwowo adzatchedwa, “anthu okanidwa ndi Yehova+ mpaka kalekale.”*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena