2 Mbiri 28:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Aedomu+ anabweranso n’kudzapha Ayuda, ndipo anagwira anthu ena n’kuwatenga. Obadiya 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa chakuti m’bale wako Yakobo unam’chitira zachiwawa,+ manyazi adzakugwira.+ Iwe udzawonongedwa ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.*+
10 Chifukwa chakuti m’bale wako Yakobo unam’chitira zachiwawa,+ manyazi adzakugwira.+ Iwe udzawonongedwa ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.*+