Levitiko 26:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Koma ngati simudzandimverabe pambuyo poona zinthu zimenezi, pamenepo ndidzakulangani mowirikiza ka 7 kuposa poyamba chifukwa cha machimo anu.+ Obadiya 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa chakuti m’bale wako Yakobo unam’chitira zachiwawa,+ manyazi adzakugwira.+ Iwe udzawonongedwa ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.*+
18 “‘Koma ngati simudzandimverabe pambuyo poona zinthu zimenezi, pamenepo ndidzakulangani mowirikiza ka 7 kuposa poyamba chifukwa cha machimo anu.+
10 Chifukwa chakuti m’bale wako Yakobo unam’chitira zachiwawa,+ manyazi adzakugwira.+ Iwe udzawonongedwa ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.*+