11 Udzanena kuti: “Ndipita kukaukira dziko lokhala ndi midzi yopanda mipanda.+ Ndipita kukaukira anthu amene akukhala mwabata, popanda chowasokoneza. Ndikaukira anthu onsewo amene akukhala m’midzi yopanda mipanda+ ndipo alibe zotsekera ndiponso zitseko.”