Ezekieli 38:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Sheba,+ Dedani,+ amalonda a ku Tarisi+ ndi mikango yawo yonse yamphamvu+ adzakufunsa kuti: “Kodi wasonkhanitsa khamu lako kuti udzalande zinthu zambiri? Kodi ukufuna kudzatenga siliva, golide, chuma ndi katundu?”’
13 “‘Sheba,+ Dedani,+ amalonda a ku Tarisi+ ndi mikango yawo yonse yamphamvu+ adzakufunsa kuti: “Kodi wasonkhanitsa khamu lako kuti udzalande zinthu zambiri? Kodi ukufuna kudzatenga siliva, golide, chuma ndi katundu?”’