Ezekieli 40:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’masomphenya a Mulungu, iye ananditengera m’dziko la Isiraeli ndi kundikhazika paphiri lalitali kwambiri.+ Mbali ya kum’mwera paphiripo panali chinachake chooneka ngati mzinda.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 40:2 Nsanja ya Olonda,3/1/1999, ptsa. 9, 119/15/1988, ptsa. 25-26
2 M’masomphenya a Mulungu, iye ananditengera m’dziko la Isiraeli ndi kundikhazika paphiri lalitali kwambiri.+ Mbali ya kum’mwera paphiripo panali chinachake chooneka ngati mzinda.+