Ezekieli 40:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kudzera mʼmasomphenya ochokera kwa Mulungu, iye ananditenga nʼkupita nane mʼdziko la Isiraeli nʼkukandikhazika paphiri lalitali kwambiri.+ Mbali yakumʼmwera paphiripo panali chinachake chooneka ngati mzinda. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 40:2 Nsanja ya Olonda,3/1/1999, ptsa. 9, 119/15/1988, ptsa. 25-26
2 Kudzera mʼmasomphenya ochokera kwa Mulungu, iye ananditenga nʼkupita nane mʼdziko la Isiraeli nʼkukandikhazika paphiri lalitali kwambiri.+ Mbali yakumʼmwera paphiripo panali chinachake chooneka ngati mzinda.