Ezekieli 40:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Chipinda chodyeramo chimene chayang’ana kumpoto ndi cha ansembe ogwira ntchito paguwa lansembe,+ omwe ndi ana a Zadoki.+ Iwo ndi ochokera mwa ana a Levi ndipo amayandikira Yehova ndi kum’tumikira.”+
46 Chipinda chodyeramo chimene chayang’ana kumpoto ndi cha ansembe ogwira ntchito paguwa lansembe,+ omwe ndi ana a Zadoki.+ Iwo ndi ochokera mwa ana a Levi ndipo amayandikira Yehova ndi kum’tumikira.”+