Ezekieli 40:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Chipinda chodyeramo chimene chayangʼana kumpoto ndi cha ansembe amene amagwira ntchito zokhudza utumiki wapaguwa lansembe,+ omwe ndi ana a Zadoki.+ Amenewa ndi Alevi amene anapatsidwa udindo woti azifika pamaso pa Yehova nʼkumamutumikira.”+
46 Chipinda chodyeramo chimene chayangʼana kumpoto ndi cha ansembe amene amagwira ntchito zokhudza utumiki wapaguwa lansembe,+ omwe ndi ana a Zadoki.+ Amenewa ndi Alevi amene anapatsidwa udindo woti azifika pamaso pa Yehova nʼkumamutumikira.”+