-
Ezekieli 41:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kunali guwa lansembe lamatabwa lalitali mikono itatu kuchokera pansi kufika pamwamba. M’litali mwake munali mikono iwiri ndipo m’makona ake munali mwa matabwa.+ M’litali mwa guwalo ndi m’mbali mwake munali mwa matabwa. Ndiyeno munthu uja anandiuza kuti: “Ili ndi tebulo limene lili pamaso pa Yehova.”+
-