Zekariya 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Masiku amenewo asanafike, anthu ndi ziweto sanali kulandira malipiro.+ Munthu wa pa ulendo, adani anali kumusowetsa mtendere,+ chifukwa ine ndinali kuyambanitsa anthu onse.’+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:10 Nsanja ya Olonda,1/1/1996, tsa. 19
10 Masiku amenewo asanafike, anthu ndi ziweto sanali kulandira malipiro.+ Munthu wa pa ulendo, adani anali kumusowetsa mtendere,+ chifukwa ine ndinali kuyambanitsa anthu onse.’+