Mateyu 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma kuti mudziwe kuti Mwana wa munthu ali ndi mphamvu padziko lapansi zokhululukira machimo+ . . .” pamenepo anauza wakufa ziwalo uja kuti: “Nyamuka, tenga kabedi kakoka uzipita kwanu.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:6 Yesu—Ndi Njira, tsa. 67 Nsanja ya Olonda,5/1/1986, tsa. 9
6 Koma kuti mudziwe kuti Mwana wa munthu ali ndi mphamvu padziko lapansi zokhululukira machimo+ . . .” pamenepo anauza wakufa ziwalo uja kuti: “Nyamuka, tenga kabedi kakoka uzipita kwanu.”+