Maliko 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma pamene akupita nanu kukakuperekani, musafulumire kuda nkhawa kuti mukanena chiyani.+ Zimene mukapatsidwe mu ola lomwelo, mukanene zimenezo, pakuti wolankhula si inu, koma mzimu woyera.+
11 Koma pamene akupita nanu kukakuperekani, musafulumire kuda nkhawa kuti mukanena chiyani.+ Zimene mukapatsidwe mu ola lomwelo, mukanene zimenezo, pakuti wolankhula si inu, koma mzimu woyera.+