Machitidwe 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo iwowa sanandipezepo m’kachisi+ ndikutsutsana ndi wina aliyense, ngakhale kuyambitsa chipolowe+ m’masunagoge kapena pena paliponse mumzindawu.
12 Ndipo iwowa sanandipezepo m’kachisi+ ndikutsutsana ndi wina aliyense, ngakhale kuyambitsa chipolowe+ m’masunagoge kapena pena paliponse mumzindawu.