Aroma 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngakhale zili choncho, si onse amene analabadira uthenga wabwino.+ Pakuti Yesaya anati: “Yehova, kodi ndani wakhulupirira zimene anamva kwa ife?”+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:16 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 11 Yesaya 2, ptsa. 198-199
16 Ngakhale zili choncho, si onse amene analabadira uthenga wabwino.+ Pakuti Yesaya anati: “Yehova, kodi ndani wakhulupirira zimene anamva kwa ife?”+