Agalatiya 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inuyo amene mukufuna kuyesedwa olungama mwa chilamulo, mwadzilekanitsa ndi Khristu,+ kaya mukhale ndani, mwagwera kunja kwa kukoma mtima kwake kwakukulu.+
4 Inuyo amene mukufuna kuyesedwa olungama mwa chilamulo, mwadzilekanitsa ndi Khristu,+ kaya mukhale ndani, mwagwera kunja kwa kukoma mtima kwake kwakukulu.+