Akolose 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho munthu asakuweruzeni+ pa nkhani ya kudya ndi kumwa+ kapena chikondwerero chinachake,+ kapenanso kusunga tsiku lokhala mwezi,+ ngakhalenso kusunga sabata,+ Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:16 Galamukani!,11/8/1992, tsa. 21 Kukambitsirana, tsa. 346
16 Choncho munthu asakuweruzeni+ pa nkhani ya kudya ndi kumwa+ kapena chikondwerero chinachake,+ kapenanso kusunga tsiku lokhala mwezi,+ ngakhalenso kusunga sabata,+