Akolose 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho musalole kuti munthu aliyense akuweruzeni chifukwa cha chakudya ndi chakumwa+ kapena chikondwerero chinachake kapenanso kusunga tsiku limene mwezi watsopano waoneka+ kapena kusunga sabata.+ Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:16 Galamukani!,11/8/1992, tsa. 21 Kukambitsirana, tsa. 346
16 Choncho musalole kuti munthu aliyense akuweruzeni chifukwa cha chakudya ndi chakumwa+ kapena chikondwerero chinachake kapenanso kusunga tsiku limene mwezi watsopano waoneka+ kapena kusunga sabata.+