1 Timoteyo 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zimayambitsanso mapokoso achiwawa pa zinthu zazing’ono pakati pa anthu opotoka maganizo+ ndi osadziwa choonadi,+ poganiza kuti kukhala wodzipereka kwa Mulungu ndi njira yopezera phindu.+ 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:5 Nsanja ya Olonda,7/15/2002, tsa. 128/15/1988, tsa. 5
5 Zimayambitsanso mapokoso achiwawa pa zinthu zazing’ono pakati pa anthu opotoka maganizo+ ndi osadziwa choonadi,+ poganiza kuti kukhala wodzipereka kwa Mulungu ndi njira yopezera phindu.+